
Spoken by 7,000,000 people in Malawi. Also spoken in Zambia, Zimbabwe, Mozambique.
Linguistic Lineage for Nyanja
Malawi -
Zambia -
Zimbabwe -
Mozambique
Atate wathu wa Kumwamba,
Mutipatse ife lero cakudya cathu calero.
From the Revised Nyanja (Union) Version of the Lord's Prayer, first edition 1922, revised 1966, published by the
Bible Society in Malawi, P.O. Box 740, Blantyre, Malawi
Dzina lanu liyeretsedwe.
Ufumu wanu udze.
Kufuna kwanu kucitidwe,
monga Kumwamba comweco pansi pano.
Ndipo mutikhululukire mangawa athu,
monga ifenso takhululukira amangawa anthu.
Ndipo musatitengere kokatiyesa,
koma mutipulumutse kwa woipayo.
Contributed by
Rev. Karin Bascom Culp - E-mail kculp@awod.com
Cifukwa cace pempherani inu comweci:
Atate wathu wa Kumwamba,
Source: "BUKU LOPATULIKA NDILO MAU A MULUNGU. Cipangano Cakale Ndi Catsopano."
Dzina lanu liyeretsedwe.
Ufumu wanu udze.
Kufuna kwanu kucitidwe,
monga Kumwamba comweco pansi pano.
Mutipatse ife lero cakudya cathu calero.
Ndipo mutikhululukire mangawa athu,
monga ifenso thakhululukira amangawa anthu.
Ndipo musatitengere kokatiyesa,
koma mutipulumutse kwa woipayo.
The Bible in Chichewa (1982)
Contributed by
Wolfgang Kuhl - E-mail WKuhl44238@aol.com

Source: "AVE MARIA in 404 lingue"
Ordine Equestro del San Sepolcro di Gerusalemme, Milano (1931).
Contributed by
David G. Landsnes, MD - E-mail dgwlmd@superlink.net
SECTION INDEX
CONVENT OF PATER NOSTER
CHRISTUS REX
© Copyright Christus Rex, Inc.